#StayHappening
Sun, 11 Apr, 2027 at 01:00 am UTC+02:00

The Winner DVD launch

  • Morningside Manor Ext 2, Sandton · Sandton
Big C Uncle Big Publisher / Host Big C Uncle Big
Share
The Winner DVD launch
Advertisement
Momo Global Entertainment And Arts
Taimon Tipa
Mambwetu
LAZZ G
Everyone Products
Sìr Marthys Prod
Cha Cha
Mikozi
Akometsi
Malawi24
Just mentioning a few..
My name is Gershom Lubanga as an artist I'm Called Big C Uncle Big..
Ndakula moyo ovutika 🥹🥹💔💔
Awa ndi mau oyambilira omwe ali pa mzere woyamba wa nyimbo yanga yomwe yimandilimbitsa mtima kwambiri kapena kuti nyimbo yomwe yinandipanga ine kukhala artist..
When I talk of kukula moyo wovutika..it's not as if I'm proud of it but I'm being greatful for my life as I mention it pa verse two kuti "You should thank almighty for your life" that's I'm alive even my life sounds more like a nightmare but I've to appreciate because life can be optional meaning that I can choose my life whether I will continue making my life miserable or have a change to better it..
Nkhani iyi imvetsetseni chonde 🥹🥹
Nyimbo zomwe ndinaimba poyamba including yomwe ndatchulayo though dzina la nyimboyo is "Taking it to another level" sizinandipanse kalikonse except chomwe ndinawinapo nkukhala artist basi koma financially I gained nothing and the worse part is I downgraded up to zero since Komwe ndinkakapeza I was spending for the recording ndipo nyimbo zikatuluka I had to pay DJs and TV presenters kuti adzindiyikira nyimbo zanga mma media koma mukudziwa lunso lapa Malawi pano limafunika kuikapo almost your fresh heart so ndinapeleka zanga zonse ndipo ndili pano..
Back to ndakula moyo ovutika.. Nkhani yikuti..
Ndikati ndakula moyo ovutika sizongomva kwa anthu kuti kuli mavuto kunja kuno koma nnaziona and I've experienced the worst in life..
Mukawerenga biography yanga on Google I mentioned to say I'm a sixth born child out of nine siblings.. imagine we were five of us sleeping pamphasa imodzi poti brother wanga wamkulu anali wamkulu and sister wina wamkulu anali atamwalira kale so five of us were using one blanket.. ndikuti anthu asanu tinkafunda chofunda chimodzi called "Chipiloni" ili linali dzina la bulangete lomwe tinkafunda lomwe silinkachapidwa chifukwa tinalibe another option or chodalira china likanyowa..
Can you imagine kugona ndima sisters akuluakulu if you think about it muona kuti life was really hard.
We were three sisters mu bulangete muja onse akuluakulu ndipo ine ndi mng'ono wanga tinali ana pomwe mng'ono wanga wina ankagona ndi mayi kuchipinda kwawo ndika sister kakang'ono kwambiri kanali kakuyamwabe by then .
GreatestHighlights that's why masiku ano ndikamati sindifunaila atsikana someone doesn't believe me.. izizi doesn't mean ndinkagonana ndima sisters angawo poti nnali mwana kwambiri koma I mean palibe chachilendo chomwe chingandipangitse kumafunsira azikazi ena kuchita kuzembela wokondedwa wanga chifukwa thupi langa silitekeseka ndi mkazi olo ataminula chamtundu wanji..
Trust me kubanja kwathu ndi kukula kwathu sitinakhaleko ndi chakudya chokwanira..
Every time when mama was cooking she always knew that we're not going to be satisfied,, she was always worried about us .
I know this but I never told her that I knew about this even when I was a kid ,, I always was worried too because my mom and dad were never happy
But here's the good thing ..
Those two worked so hard that we survived..🙏🙏

My whole childhood.. I never wore good clothes where I can't mention of shoes..
Ndinamvala nsapato yoyamba nnali STD 4 and I was 10 years old.. nsapato ya plastic called "gondola" nsapato iyi kuivala opanda sokosi inkacheka kwambiri ndipo inkangovalidwa bwino kukakhala dzuwa kuti ifeweko isandipange zilonda and my father was very happy and proud kuti andigulira nsapato..
I never had a luxury life.. I and my siblings grew up that life yoti kungokumbukira ndimakhetsa misozi ndipo olo nditatopa chamtundu wanji ndimadzadzidwa ndi mphamvu zoopsa chifukwa sindifuna kubwelerako Komwe ndichokerako ndipo pano ndine bambo wa anthu ena omwe sindikhumbira kuti akule ngati momwe ndinakuika ine I pray in Jesus name.
Chonde mveraniko nyimbo yanga "Taking it to another level" by Big C Uncle Big in all streaming platforms across the world
Taking it to another level ndi nyimbo yomwe ndinaimba kuchoka pansi pa mtima wanga and that song is my life of which I know kuti Malawi as a poor country ambiri akula ngati ine ndipo ndikukambamu nzoti ena akuvutika and nyimboyo inde ndinaimba talking about me koma I'm speaking on behalf of others too moti ndi chikhulupiriro chonse kuti our tomorrow is better than yesterday..
Pano ndili ndi launch kuno ku Johannesburg pomwe ndikutulutsa album yanga called the winner ndipo ndidzailongosolanso
#takingittoanotherlevel
#Thewinner
Advertisement

Event venue

Morningside Manor Ext 2, Sandton, South Africa

Tickets
Concerts, fests, parties, meetups — all the happenings, one place.

Discover more events by tag

Ask AI if this event suits you

Keep the plans coming

More events in Sandton

Feed A Million Meals

Thu, 15 Apr at 01:55 pm Kelvin Dr &, Bowling Ave, Morningside Manor, Sandton, South Africa

Sandton is happening.

See everything else that’s on — concerts, markets, comedy and more.